-
Genesis 1:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mulungu analenga nyama zikuluzikulu zamʼnyanja ndi zamoyo zonse zokhala mʼmadzi mogwirizana ndi mitundu yake. Analenganso chamoyo chilichonse chouluka mogwirizana ndi mtundu wake. Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.
-