Genesis 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu atatero, anazidalitsa ponena kuti: “Muswane ndipo muchulukane nʼkudzaza nyanja zonse.+ Ndipo zamoyo zouluka zichuluke padziko lapansi.” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 Galamukani!,3/2014, tsa. 7
22 Mulungu atatero, anazidalitsa ponena kuti: “Muswane ndipo muchulukane nʼkudzaza nyanja zonse.+ Ndipo zamoyo zouluka zichuluke padziko lapansi.”