Genesis 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Mulungu anati: “Dziko lapansi likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta, nyama zokwawa,* komanso nyama zakutchire monga mwa mitundu yake.”+ Ndipo zinaterodi.
24 Kenako Mulungu anati: “Dziko lapansi likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta, nyama zokwawa,* komanso nyama zakutchire monga mwa mitundu yake.”+ Ndipo zinaterodi.