Genesis 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abulamu akubwera kuchokera kumene anagonjetsa Kedorelaomere limodzi ndi mafumu amene anali naye, mfumu ya ku Sodomu inapita kukakumana naye kuchigwa cha Save, kapena kuti chigwa cha Mfumu.+
17 Abulamu akubwera kuchokera kumene anagonjetsa Kedorelaomere limodzi ndi mafumu amene anali naye, mfumu ya ku Sodomu inapita kukakumana naye kuchigwa cha Save, kapena kuti chigwa cha Mfumu.+