-
Genesis 26:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako Abimeleki anauza Isaki kuti: “Uchoke kwathu kuno, chifukwa wakhala munthu wamphamvu kwambiri kuposa ifeyo.”
-