Genesis 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma iwo anayankha kuti: “Ife taona kuti Yehova ali ndi iwe.+ Choncho tinaganiza zokupempha kuti, ‘tilumbire kuti pakati pa iwe ndi ife pakhale mtendere ndipo tichite nawe pangano.+
28 Koma iwo anayankha kuti: “Ife taona kuti Yehova ali ndi iwe.+ Choncho tinaganiza zokupempha kuti, ‘tilumbire kuti pakati pa iwe ndi ife pakhale mtendere ndipo tichite nawe pangano.+