Ekisodo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni chifukwa mwachititsa kuti Farao ndi atumiki ake aipidwe nafe,* moti mwawapatsa lupanga mʼmanja mwawo kuti atiphe.”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:21 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 15
21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni chifukwa mwachititsa kuti Farao ndi atumiki ake aipidwe nafe,* moti mwawapatsa lupanga mʼmanja mwawo kuti atiphe.”+