Ekisodo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi. Amenewa anali mabanja a Alevi mogwirizana ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+
19 Ndipo ana aamuna a Merari anali Mali ndi Musi. Amenewa anali mabanja a Alevi mogwirizana ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+