Ekisodo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndidzalola kuti Farao aumitse mtima wake,+ ndipo adzawathamangira. Ndidzalemekeza dzina langa pogonjetsa Farao ndi gulu lake lonse lankhondo,+ ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Choncho Aisiraeli anachitadi zomwezo.
4 Ine ndidzalola kuti Farao aumitse mtima wake,+ ndipo adzawathamangira. Ndidzalemekeza dzina langa pogonjetsa Farao ndi gulu lake lonse lankhondo,+ ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Choncho Aisiraeli anachitadi zomwezo.