Ekisodo 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndilola kuti Aiguputo aumitse mitima yawo, moti atsatira Aisiraeli panyanjapo. Ndichita zimenezi kuti ndilemekeze dzina langa pogonjetsa Farao, gulu lake lonse lankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+
17 Koma ine ndilola kuti Aiguputo aumitse mitima yawo, moti atsatira Aisiraeli panyanjapo. Ndichita zimenezi kuti ndilemekeze dzina langa pogonjetsa Farao, gulu lake lonse lankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+