Ekisodo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+
3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+