Levitiko 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Musamapemphe anthu olankhula ndi mizimu+ kuti akuthandizeni ndipo musamafunse malangizo kwa anthu olosera zamʼtsogolo+ nʼkukuchititsani kukhala odetsedwa. Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:31 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 24
31 Musamapemphe anthu olankhula ndi mizimu+ kuti akuthandizeni ndipo musamafunse malangizo kwa anthu olosera zamʼtsogolo+ nʼkukuchititsani kukhala odetsedwa. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.