Levitiko 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nʼchifukwa chake ndinakuuzani kuti: “Inuyo mudzatenga dzikolo ndipo ine ndidzalipereka mʼmanja mwanu kuti likhale lanu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndakupatulani kwa anthu a mitundu ina.”+
24 Nʼchifukwa chake ndinakuuzani kuti: “Inuyo mudzatenga dzikolo ndipo ine ndidzalipereka mʼmanja mwanu kuti likhale lanu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndakupatulani kwa anthu a mitundu ina.”+