Levitiko 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndidzaika mantha mʼmitima ya anthu amene adzapulumuke+ omwe akukhala mʼdziko la adani awo, moti adzathawa phokoso la tsamba louluka. Iwo adzathawa ngati munthu amene akuthawa lupanga, moti adzagwa popanda wowathamangitsa.+
36 Ndidzaika mantha mʼmitima ya anthu amene adzapulumuke+ omwe akukhala mʼdziko la adani awo, moti adzathawa phokoso la tsamba louluka. Iwo adzathawa ngati munthu amene akuthawa lupanga, moti adzagwa popanda wowathamangitsa.+