Numeri 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Asilikali onse a gulu la Yuda amene analembedwa mayina alipo 186,400. Amenewa azikhala oyamba kunyamuka.+
9 Asilikali onse a gulu la Yuda amene analembedwa mayina alipo 186,400. Amenewa azikhala oyamba kunyamuka.+