Numeri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma chofunika nʼchakuti musapandukire Yehova, ndipo anthu amʼdzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo, koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope.” Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:9 Nsanja ya Olonda,10/1/2006, tsa. 17
9 Koma chofunika nʼchakuti musapandukire Yehova, ndipo anthu amʼdzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo, koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope.”