Numeri 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzikaperekanso vinyo kuti akhale nsembe yachakumwa. Azikakhala wokwana gawo limodzi mwa magawo 4 a muyezo wa hini. Vinyoyo muzikamupereka limodzi ndi nsembe yopsereza,+ kapena ndi nsembe ya mwana wa nkhosa wamphongo.
5 Muzikaperekanso vinyo kuti akhale nsembe yachakumwa. Azikakhala wokwana gawo limodzi mwa magawo 4 a muyezo wa hini. Vinyoyo muzikamupereka limodzi ndi nsembe yopsereza,+ kapena ndi nsembe ya mwana wa nkhosa wamphongo.