Numeri 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zopereka zonse zopatulika zimene Aisiraeli azipereka kwa Yehova,+ ndakupatsa iwe ndi ana ako aamuna ndi aakazi, kuti likhale gawo lanu mpaka kalekale.+ Limeneli ndi pangano lamuyaya lamchere* limene Yehova akupanga ndi iwe komanso mbadwa zako.”
19 Zopereka zonse zopatulika zimene Aisiraeli azipereka kwa Yehova,+ ndakupatsa iwe ndi ana ako aamuna ndi aakazi, kuti likhale gawo lanu mpaka kalekale.+ Limeneli ndi pangano lamuyaya lamchere* limene Yehova akupanga ndi iwe komanso mbadwa zako.”