Deuteronomo 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Chifukwa choti ankakonda makolo anu ndipo anasankha mbadwa* zawo zobwera pambuyo pawo,+ anakutulutsani ku Iguputo ndi mphamvu zake zazikulu ndipo ankakuyangʼanirani.
37 Chifukwa choti ankakonda makolo anu ndipo anasankha mbadwa* zawo zobwera pambuyo pawo,+ anakutulutsani ku Iguputo ndi mphamvu zake zazikulu ndipo ankakuyangʼanirani.