Deuteronomo 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Yehova anayandikira kwa makolo anu okha nʼkuwasonyeza chikondi chake, ndipo wasankha inuyo mbadwa zawo+ pakati pa anthu onse, ngati mmene mulili lero.
15 Koma Yehova anayandikira kwa makolo anu okha nʼkuwasonyeza chikondi chake, ndipo wasankha inuyo mbadwa zawo+ pakati pa anthu onse, ngati mmene mulili lero.