21 Ngati malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuikapo dzina lake+ adzakhale kutali kwambiri ndi inu, muzidzapha zina mwa ngʼombe zanu kapena nkhosa zanu zimene Yehova wakupatsani, mogwirizana ndi zimene ndakulamulani, ndipo nyamazo muzidzadyera mumzinda wanu nthawi iliyonse imene mukufuna.