Deuteronomo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+
2 Chifukwa ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+