Deuteronomo 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova Mulungu wanu wamusankha pamodzi ndi ana ake, pakati pa mafuko anu onse, kuti atumikire mʼdzina la Yehova nthawi zonse.+
5 Yehova Mulungu wanu wamusankha pamodzi ndi ana ake, pakati pa mafuko anu onse, kuti atumikire mʼdzina la Yehova nthawi zonse.+