Deuteronomo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+
21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+