Deuteronomo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngati mwamuna wapezeka akugona ndi mkazi wa mwiniwake, onse awiri, mwamuna amene amagona ndi mkaziyo komanso mkaziyo, azifera limodzi.+ Choncho muzichotsa oipawo mu Isiraeli.
22 Ngati mwamuna wapezeka akugona ndi mkazi wa mwiniwake, onse awiri, mwamuna amene amagona ndi mkaziyo komanso mkaziyo, azifera limodzi.+ Choncho muzichotsa oipawo mu Isiraeli.