-
Deuteronomo 24:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 mwamuna woyamba amene anamuthamangitsa uja sadzaloledwa kumutenganso kuti akhale mkazi wake pambuyo poti waipitsidwa, chifukwa zimenezo ndi zonyansa kwa Yehova. Musamachite machimo amenewa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa.
-