Deuteronomo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati mwapereka ngongole ya mtundu uliwonse kwa mnzanu,+ musamalowe mʼnyumba yake kukatenga chimene wanena kuti akupatsani kuti chikhale chikole.
10 Ngati mwapereka ngongole ya mtundu uliwonse kwa mnzanu,+ musamalowe mʼnyumba yake kukatenga chimene wanena kuti akupatsani kuti chikhale chikole.