Deuteronomo 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Abambo asamaphedwe chifukwa cha zimene ana awo achita, ndipo ana asamaphedwe chifukwa cha zimene abambo awo achita.+ Munthu aliyense aziphedwa chifukwa cha tchimo lake.+
16 Abambo asamaphedwe chifukwa cha zimene ana awo achita, ndipo ana asamaphedwe chifukwa cha zimene abambo awo achita.+ Munthu aliyense aziphedwa chifukwa cha tchimo lake.+