Deuteronomo 28:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mudzalima nʼkudzala mitengo ya mpesa, koma simudzakolola mphesa zake nʼkumwa vinyo,+ chifukwa mbozi zidzadya mpesawo. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:39 Nsanja ya Olonda,6/15/2006, tsa. 18
39 Mudzalima nʼkudzala mitengo ya mpesa, koma simudzakolola mphesa zake nʼkumwa vinyo,+ chifukwa mbozi zidzadya mpesawo.