Deuteronomo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri. Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+
2 Iye anati: “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri. Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+