Yoswa 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe amene adzakugonjetse masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe ngati mmene ndinakhalira ndi Mose+ ndipo sindidzakutaya kapena kukusiya.+
5 Palibe amene adzakugonjetse masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe ngati mmene ndinakhalira ndi Mose+ ndipo sindidzakutaya kapena kukusiya.+