Yoswa 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Malire a gawo la fuko la Manase anayambira ku Aseri kukafika ku Mikametatu,+ patsogolo pa Sekemu.+ Malirewo analowera kumʼmwera* kukafika kwa anthu okhala ku Eni-Tapuwa.
7 Malire a gawo la fuko la Manase anayambira ku Aseri kukafika ku Mikametatu,+ patsogolo pa Sekemu.+ Malirewo analowera kumʼmwera* kukafika kwa anthu okhala ku Eni-Tapuwa.