Yoswa 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchigawo cha Yorodano, kumʼmawa kwa Yeriko, anasankha Bezeri,+ mʼchipululu cha mʼdera lokwererapo la fuko la Rubeni. Anasankhanso Ramoti+ ku Giliyadi mʼdera la fuko la Gadi komanso Golani+ ku Basana mʼdera la fuko la Manase.+
8 Kuchigawo cha Yorodano, kumʼmawa kwa Yeriko, anasankha Bezeri,+ mʼchipululu cha mʼdera lokwererapo la fuko la Rubeni. Anasankhanso Ramoti+ ku Giliyadi mʼdera la fuko la Gadi komanso Golani+ ku Basana mʼdera la fuko la Manase.+