Yoswa 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anachita maere ena, ndipo Akohati amene anatsala anawapatsa mizinda 10 yochokera mʼmabanja a fuko la Efuraimu,+ la Dani ndi hafu ya fuko la Manase.+
5 Anachita maere ena, ndipo Akohati amene anatsala anawapatsa mizinda 10 yochokera mʼmabanja a fuko la Efuraimu,+ la Dani ndi hafu ya fuko la Manase.+