-
Oweruza 6:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Komabe, Gidiyoni anauza Mulungu woona kuti: “Musandikwiyire chonde, ndiloleni ndipemphenso kamodzi kokha. Chonde ndiloleni ndikuyeseninso kamodzi kokha ndi ubweyawu. Ubweya wokhawu ukhale wouma, koma nthaka yonse inyowe ndi mame.”
-