Oweruza 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Olamulira a Afilisiti anasonkhana kuti apereke nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo komanso kuti achite chikondwerero, popeza ankanena kuti: “Mulungu wathu watipatsa mdani wathu Samisoni!” Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:23 Nsanja ya Olonda,7/15/2003, tsa. 25
23 Olamulira a Afilisiti anasonkhana kuti apereke nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo komanso kuti achite chikondwerero, popeza ankanena kuti: “Mulungu wathu watipatsa mdani wathu Samisoni!”