-
1 Samueli 3:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Yehova anamuitananso kuti: “Samueli!” Ndiyeno Samueli anadzuka nʼkupitanso kwa Eli kukanena kuti: “Ndabwera chifukwa ndamva mukundiitana.” Koma Eli anamuuza kuti: “Sindinakuitane mwana wanga. Pita ukagone.”
-