1 Samueli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake mpaka kalekale chifukwa cha zinthu zolakwika zimene iye akuzidziwa.+ Ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+
13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake mpaka kalekale chifukwa cha zinthu zolakwika zimene iye akuzidziwa.+ Ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+