3 Ukakachoka pamenepo ukapitirize ulendo wako mpaka ukafike kumtengo waukulu wa ku Tabori. Kumeneko ukakumana ndi amuna atatu akupita ku Beteli+ kukalambira Mulungu woona. Mmodzi akhala atanyamula ana atatu a mbuzi, wina atanyamula mikate itatu ndipo winayo atanyamula mtsuko waukulu wa vinyo.