-
1 Samueli 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ukakachoka pamenepo, ukafika kuphiri la Mulungu woona, kumene kukukhala asilikali a Afilisiti. Ukakafika mumzinda ukakumana ndi kagulu ka aneneri akuchokera kumalo okwezeka, akulosera. Patsogolo pawo pakakhala anthu oimba maseche, chitoliro, zeze ndi choimbira cha zingwe.
-