1 Samueli 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 (Ahiya ndi amene ankanyamula efodi.+ Iye anali mwana wa Ahitubu,+ mchimwene wa Ikabodi,+ mwana wa Pinihasi,+ mwana wa Eli+ yemwe anali wansembe wa Yehova ku Silo.)+ Koma anthu sanadziwe kuti Yonatani wachoka.
3 (Ahiya ndi amene ankanyamula efodi.+ Iye anali mwana wa Ahitubu,+ mchimwene wa Ikabodi,+ mwana wa Pinihasi,+ mwana wa Eli+ yemwe anali wansembe wa Yehova ku Silo.)+ Koma anthu sanadziwe kuti Yonatani wachoka.