1 Samueli 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sauli anayankha kuti: “Zachokera kwa Aamaleki. Anthuwa sanaphe* nkhosa ndi ngʼombe zabwino kwambirizi kuti ziperekedwe nsembe kwa Yehova Mulungu wanu. Koma zina zonse zotsala taziwononga.”
15 Sauli anayankha kuti: “Zachokera kwa Aamaleki. Anthuwa sanaphe* nkhosa ndi ngʼombe zabwino kwambirizi kuti ziperekedwe nsembe kwa Yehova Mulungu wanu. Koma zina zonse zotsala taziwononga.”