1 Samueli 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Samueli anati: “Ndipita bwanji? Sauli akamva andipha ndithu.”+ Atatero, Yehova anamuuza kuti: “Popita utenge ngʼombe yaikazi yaingʼono ndipo ukanene kuti, ‘Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova.’
2 Koma Samueli anati: “Ndipita bwanji? Sauli akamva andipha ndithu.”+ Atatero, Yehova anamuuza kuti: “Popita utenge ngʼombe yaikazi yaingʼono ndipo ukanene kuti, ‘Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova.’