17 Kenako Sauli anauza Davide kuti: “Paja ndili ndi mwana wamkazi wamkulu, Merabu,+ ndipo ndidzakupatsa kuti akhale mkazi wako.+ Koma iweyo upitirize kumenya nkhondo za Yehova+ ndiponso kundisonyeza kuti ndiwe wolimba mtima.” Mumtima mwake ankati: ‘Ndisamuphe ndine koma amuphe ndi Afilisiti.’+