1 Samueli 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Davide anapita ku Mizipe, ku Mowabu ndipo anauza mfumu ya Mowabu+ kuti: “Ndikupempha kuti bambo ndi mayi anga azikhala nawo kuno mpaka nditadziwa zimene Mulungu andichitire.”
3 Kenako Davide anapita ku Mizipe, ku Mowabu ndipo anauza mfumu ya Mowabu+ kuti: “Ndikupempha kuti bambo ndi mayi anga azikhala nawo kuno mpaka nditadziwa zimene Mulungu andichitire.”