1 Samueli 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Pa atumiki anu onse ndi ndani ali wokhulupirika* ngati Davide?+ Iye ndi mkamwini wa mfumu,+ mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka mʼnyumba yanu.+
14 Ahimeleki anayankha mfumuyo kuti: “Pa atumiki anu onse ndi ndani ali wokhulupirika* ngati Davide?+ Iye ndi mkamwini wa mfumu,+ mtsogoleri wa asilikali okulonderani ndiponso munthu wolemekezeka mʼnyumba yanu.+