1 Samueli 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Davide anauza Abiyatara kuti: “Tsiku lomwe lija+ nditangoona kuti Doegi wa ku Edomu aliko, ndinadziwa kuti akauza Sauli. Ineyo ndi amene ndachititsa kuti anthu onse amʼnyumba ya bambo ako aphedwe.
22 Ndiyeno Davide anauza Abiyatara kuti: “Tsiku lomwe lija+ nditangoona kuti Doegi wa ku Edomu aliko, ndinadziwa kuti akauza Sauli. Ineyo ndi amene ndachititsa kuti anthu onse amʼnyumba ya bambo ako aphedwe.