1 Samueli 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Sauli anauza atumiki ake kuti: “Ndifufuzireni mzimayi amene amalankhula ndi mizimu+ kuti ndikaonane naye.” Atumiki akewo anamuuza kuti: “Ku Eni-dori+ kuli mzimayi amene amalankhula ndi mizimu.”
7 Kenako Sauli anauza atumiki ake kuti: “Ndifufuzireni mzimayi amene amalankhula ndi mizimu+ kuti ndikaonane naye.” Atumiki akewo anamuuza kuti: “Ku Eni-dori+ kuli mzimayi amene amalankhula ndi mizimu.”