2 Samueli 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anapha Mfilisitiyo. Zitatero asilikali a Davide anamulumbirira kuti: “Musamapitenso ndi ife kunkhondo.+ Musazimitse nyale ya Isiraeli.”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:17 Nsanja ya Olonda,1/15/2013, ptsa. 30-31
17 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anathandiza+ Davide ndipo anapha Mfilisitiyo. Zitatero asilikali a Davide anamulumbirira kuti: “Musamapitenso ndi ife kunkhondo.+ Musazimitse nyale ya Isiraeli.”+