1 Mafumu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Solomo ankalamulira maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti nʼkukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumuwa ankabweretsa msonkho kwa Solomo komanso kumutumikira kwa moyo wake wonse.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:21 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 16
21 Solomo ankalamulira maufumu onse kuyambira ku Mtsinje*+ mpaka kudziko la Afilisiti nʼkukafika kumalire ndi Iguputo. Maufumuwa ankabweretsa msonkho kwa Solomo komanso kumutumikira kwa moyo wake wonse.+